Pena Lyrics by HD ENTERTAINMENT


Pena ngati ungogona usadzukenso
Pena ngati zachikondi uiwaleko
Pena ngati ungoledzera aaaah aah aah
Pena ngati ugome kumowa eh
Nanga ndifere chikondi?
Mpaka ndionde chonchi?
Anthu milibe chisoni eh
Nanga ndifere chikondi?
Mpaka ndionde chonchi?
Anthu milibe chisoni eh yeah eh

Pena ngati ndigonziiwala ine
Pena ngati ndingozitaya ine
Cos love hurts, love hurts
Chikondi chikuwawa iwe, Chikondi chikuwawa iwe
Pena ngati ndapepetulidwa ine eh he
Sad songs i
Can’t get rid of these sad songs
Girl, I still see your face
I’m still on your case
Mesa munkati simudzachoka  
Mesa munkati siudzasowa
Where are you now?
Where are you now that I need you yah!
Pena ngati ndigonziiwala ine
Pena ngati ndingozitaya ine
Cos love hurts, love hurts
Chikondi chikuwawa iwe, Chikondi chikuwawa iwe
Pena ngati ndapepetulidwa ine eh he

I thought it won’t be the same
I thought it won’t be the same
I thought you were different from the other girl that I met before
I thought it won’t be the same
I thought it won’t be the same
Koma no no, no no,  no no
Pena ngati ndigonziiwala ine
Pena ngati ndingozitaya ine
Cos love hurts, love hurts
Chikondi chikuwawa iwe, Chikondi chikuwawa iwe
Pena ngati ndapepetulidwa ine eh he
Pena ngati ndigonziiwala ine
Pena ngati ndingozitaya ine
Cos love hurts, love hurts
Chikondi chikuwawa iwe, Chikondi chikuwawa iwe
Pena ngati ndapepetulidwa ine eh he

Watch Video

About Pena

Album : Pena (Single)
Release Year : 2020
Added By : Farida
Published : Oct 19 , 2020

More HD ENTERTAINMENT Lyrics

Comments ( 0 )

No Comment yet



About AfrikaLyrics

Afrika Lyrics is the most diverse collection of African song lyrics and translations. Afrika Lyrics provides music lyrics from over 30 African countries and lyrics translations from over 10 African Languages into English and French

Follow Afrika Lyrics

© 2024, We Tell Africa Group Sarl