Basi Lyrics
Basi Lyrics by KELL KAY
You already know
Pa iwe basi
Pa iwe basi
Pa iweyo ndidathela
Ndamaliza masewela
Pa iwe basi
Pa iwe basi
Pa iweyo ndidathela
Ndamaliza masewela
Call me Inkosi
Wankasi mmodzi
Ambiri ngozi
Wanga ndimmodzi
Osavela za mikozi
Vela apongozi
Sizakutututsa msodzi
Tiye ku jozi
One girl for me
One girl for me now
Nali ngati mlenje
Ndamusaka ndekha
Bwelani nkozi, Imani phozi
Inu ndankhoswe, tavanani chimodzi
Nnanena kale sinzakusiya mmalelele
Olo nyumba mwanga suzadyela thelele
Suzozubana malaku phelele
Chikondi change nde uchimvelele hey
Pa iwe basi
Pa iwe basi
Pa iweyo ndidathela
Ndamaliza masewela
Pa iwe basi
Pa iwe basi
Pa iweyo ndidathela
Ndamaliza masewela
Za jingle janga zawana
Izi ndapanga padzana
Nde sarafina ayi ayi
Zachibwana pano ayi, aaaaayiii
Am with you mama wee
Sinzakutaya, sinzakuthawa,sinzakuswaya
Usade nkhawa mama wee
Fall in love, fall in love, fall in love
Feels so good to fall in love, fall in love
Maka ukagwa ndi amene umankonda
Mawa podzuka ndi chimwemwe chokhachokha
Pa iwe basi
Pa iwe basi
Pa iweyo ndidathela
Ndamaliza masewela
Pa iwe basi
Pa iwe basi
Pa iweyo ndidathela
Ndamaliza masewela
Watch Video
About Basi
More KELL KAY Lyrics
Comments ( 0 )
No Comment yet
You May also Like
Get Afrika Lyrics Mobile App
About AfrikaLyrics
Follow Afrika Lyrics
© 2025, We Tell Africa Group Sarl