Pano Lyrics
Pano Lyrics by DRIEMO
Is this a joke
Are you kidding me
Utanthauza chan
Zachuluka ndi nkhani you're planning to leave me
Am I a fool
For falling for you
Tadutsa mu zambiri
Tapanga ndi Zambiri
Now you want to switch like dat
Kodi ndayipa pano
Ndakubhowa pano
Zonse zija wandichititsa zikayipe pano
Ooh Kodi ndayipa pano
Ndakubhowa pano
Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero
Unandiyambitsa shisha mowa mesa ndiwe
Iwe na ine muma club everyday
Lero ukut khalidwe LA banja mwa ine
Kodi ndi game yantundu wanji you're playing
Nde unkandisinthiranji
Sinthiranji
Nde unkandisinthiranji... Oh my God
Fees yako itashupha ndinagulitsa munda ine
Lero munagwidwa ndi shasha
Ati ine ndiwakumunda oooh
Koma izizi ndinkapanga chifukwa ndimasamala za iwe
Ineyo ndinkablunder kufuna kukusangalatsa iwe
How I wish I could go back
How I wish I could rewind
How I wish I could fall back
But it's too late
Too late
Kodi ndayipa pano
Ndakubhowa pano
Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero
Unandiyambitsa shisha mowa mesa ndiwe
Iwe na ine muma club everyday
Lero ukut khalidwe LA banja mwa ine
Kodi ndi game yantundu wanji you're playing
Nde unkandisinthiranji
Sinthiranji
Nde unkandisinthiranjiii
Oh my God
Zomwe mutandi siyire pano
Ndizomwe mudandiphunzitsa
Zomwe mutanditukwane nazo pano
Ndizomwe mudandidziwitsaaa iiiiiiineeeeeee
Unandiyambitsa shisha mowa mesa ndiwe
Iwe na ine muma club everyday
Lero ukut khalidwe LA banja mwa ine
Kodi ndi game yantundu wanji you're playing
Nde unkandisinthiranji
Watch Video
About Pano
More DRIEMO Lyrics
Comments ( 0 )
No Comment yet
You May also Like
Get Afrika Lyrics Mobile App
About AfrikaLyrics
Follow Afrika Lyrics
© 2024, We Tell Africa Group Sarl