PHYZIX Chikondi cover image

Chikondi Lyrics

Chikondi Lyrics by PHYZIX


M'bobo dem Ayayayaya
Phyzix Very Good, Very Good
Ndimangomvera ma romours
Macia Ati love is sweet
Yeah Very Good, Very Good

Zimakhala bwino kumakhala 2-2
Umumu ndi momwe tinalengedwela anthu
Ndinaipeza nthiti yanga ndine thunthu
Umandikwanira real love is what am into
Baby girl Chikondi osabisa ndimakunyadila daily kumakukissa mtswaaah
Osamachoka ndimakumisa umandidalitsa
When I think of an Angel you the picture
Umandibweletsera mtendere wodabwitsa
Wanna make sure kuti nthawi ndakupatsa
Olo anthu atanena kuti ndinapusa

Ndimangomva ma romours
Ati love is sweet
Ndimagwidwa ndi nthumazi yeeeee mwina nkudzathera misonzi

Ngati ndalama zikhale
Kaya kutchuka kukhale
Kukongora kukhale
U handsome ukhaleeee
Nane ndimafuna chikondi
Nane ndimafuna kukondedwa
Nane ndimasowa chikondi
Nane ndimafuna kukondedwa
Oyayaya

Let's make everyday Valentine's Day
Tizikondana and not care what people say
Zaka kumapita koma same way/ baby girl you my sunshine let's make hay
As your man I promise to love you
To always be gentle popanda za ganyavu
I know many guys wanna cuff you
Tiye tizivaya padeni ngati ndi curfew
Dancing to the rhythm of a love song
Amene akuti tidzasiyanawo they dead wrong
The smiles the frowns/ the ups and the downs
Chikondi sichophweka we just gotta be strong

Ndimangomva ma romours
Ati love is sweet
Ndimagwidwa ndi nthumazi yeeeee mwina nkudzathera misonzi

Ngati ndalama zikhale
Kaya kutchuka kukhale
Kukongora kukhale
U handsome ukhaleeee
Nane ndimafuna chikondi
Nane ndimafuna kukondedwa
Nane ndimasowa chikondi
Nane ndimafuna kukondedwa
Oyayaya

Put aside your pride iwe mwamuna wanga mkazi wanga
Kuzitukumula kuononga zinthu mama ayaaa
Iyaaaaaa yeeeeeheeeee

Ngati ndalama zikhale
Kaya kutchuka kukhale
Kukongora kukhale
U handsome ukhaleeee
Nane ndimafuna chikondi
Nane ndimafuna kukondedwa
Nane ndimasowa chikondi
Nane ndimafuna kukondedwa
Oyayaya

Watch Video

About Chikondi

Album : Chikondi (Single)
Release Year : 2022
Copyright : © 2022 It's Only Entertainment (IOE)
Added By : Farida
Published : Feb 01 , 2022

More PHYZIX Lyrics

PHYZIX
PHYZIX

Comments ( 0 )

No Comment yet



About AfrikaLyrics

Afrika Lyrics is the most diverse collection of African song lyrics and translations. Afrika Lyrics provides music lyrics from over 30 African countries and lyrics translations from over 10 African Languages into English and French

Follow Afrika Lyrics

© 2025, We Tell Africa Group Sarl