Sugar Lyrics by NAMADINGO


Na na na na
Namadingo oh
Oh na na
Oh na na

I’ve been here before
Izi zimandiuphya
When I remember this thing
Nivelela mantha
Falling in love ndintima wonse
But in return cheating on me
Kudinamiza aaaa
Ndinkakanika kugona
All night talking to myself
Kumadzifunsa, ndikupelewela pati
Ine zimenezo ayi

Nkhani ya chikundi, nkhani ya chiku ooo
Nkhani ya chikondi
Ine ndikufuna ndidzinva sugar
Nkhani ya chikondi, nkhani ya chiko ooo
Nkhani ya chikondi
Ine ndikufuna ndidzinva sugar
Sugar sugar
Bring me sugar
Na na na na na
Namadingo

When I give myself to love
There is no holding back yeh
No looking back mmmh
All the time I gat your back
But when you loose me I’m never coming back
Chifukwa ine ndimadzipeleka aah
Kuja kothelatu
Ukandisiya ngati ntima susweka
For sure ung’ambika
Sindimafuna kudzamva phuma
Ngati mwina ndiphulika
I don’t want that life
I just want sweet love
For the Bible says
Mukonde nzako momwe, udzikondela mwini

Nkhani ya chikondi
Nkhani ya chiko ooo
Nkhani ya chikondi
Ine ndikufuna ndidzinya sugar
Nkhani ya chiko
Nkhani ya chiko ooo
Nkhani ya chiko
Nkhani ya chiko
Story ya chiko oo
Nkhani ya chikondi
Ine ndikufuna ndidzinya sugar
Kufilinga sugar, sugar
Bring me sugar

Watch Video

About Sugar

Album : Sugar (Single)
Release Year : 2022
Added By : Farida
Published : May 07 , 2022

More NAMADINGO Lyrics

NAMADINGO

Comments ( 0 )

No Comment yet



About AfrikaLyrics

Afrika Lyrics is the most diverse collection of African song lyrics and translations. Afrika Lyrics provides music lyrics from over 30 African countries and lyrics translations from over 10 African Languages into English and French

Follow Afrika Lyrics

© 2024, We Tell Africa Group Sarl