Paroles de Mdalitso
Paroles de Mdalitso Par PIKSY
Piksy Mdalitso lyrics video
Mtima wanga udzavutika
Ndikayang’anira zonse zochitika ah
Ndikayesetsa kusangalatsa aliyense
Pochita zinthu ndidzatsutsika
Kuthekera k wanga konse kubisika ah
Ndikayesetsa kusangalatsa aliyense
Zoona za mmoyo
Umafunabe nzako okugwira mkono
Pamene zako zada mwina wagwa
Akuthandize kudzuka
Komabe ndaudziwa moyo
Sionse agathe kugwira mkono
Nzosatheka kukondweretsa
Ambuye chomwe ndipempha
[CHORUS]
Ndifuna ndikhale m’dalitso
Kwaonse okonda ni ozonda
Ndifuna ndikhale m’dalitso
Kwaonse okonda ni ozonda
Ndikhale m’dalitso ouh ooh ouh eh
Ndikhale m’dalitso ouh ooh ouh eh
Nseu wanga udzakumbika
Komwe ndikupita ndzakanika kufika
Ndikayesetsa kusangalatsa aliyense …aliyense eeh
Mtsinje wanga ndidzaumitsa
Chomwe ndachigwira mmanja adzaphumitsa
Ndikayesetsa kusangalatsa aliyense …aliyense eeh
Sichirichonse chomwe tikonda
Akachiona ena akondwa
Ena amafuna titagwa
Kutiona zathu zitada …Eeh
Koma count it all joy
Izi nzazing’ono …Noo
Nzosatheka kukondweretsa
Alyinse ambuye chomwe ndipempha
[CHORUS]
Ndifuna …Ndikhale …M’dalitso
Kwaonse okonda ndi ozonda
Ndifuna …Ndikhale …M’dalitso
Kwaonse okonda ndi ozonda
Ndikhale m’dalitso ouh ooh
Ndikhale m’dalitso ouh ooh
Ndifuna …Ndikhale …M’dalitso (m’dalitso)
Kwaonse okonda ndi ozonda (ozonda)
Ndikhale m’dalitso ouh ooh
Ndifuna …Ndikhale …M’dalitso (m’dalitso)
Kwaonse okonda ndi ozonda
Ndikhale m’dalitso ouh ooh
Ndifuna …Ndikhale …M’dalitso (m’dalitso)
Kwaonse okonda ndi ozonda
Ndikhale m’dalitso ouh ooh
Ndifuna …Ndikhale …M’dalitso
Kwaonse okonda ndi ozonda
Ndikhale m’dalitso ouh ooh
Ecouter
A Propos de "Mdalitso"
Plus de Lyrics de PIKSY
Commentaires ( 0 )
Aucun commentaire pour l'instant
Vous aimeriez sûrement
Essayez l'application Mobile
A propos de AfrikaLyrics
Suivre Afrika Lyrics
© 2025, We Tell Africa Group Sarl