Good Bye Lyrics
Good Bye Lyrics by EM SPECIAL
Mi Seh I feel so lonely
Without you my baby
Ilo ndi bodza loti sitimamvana
Iwe ndi wanga tikamauzana
Ukamatalikila (ukamatalikila)
Uzindiganizila monga ndimachitila
Ukamatalikila uzindiganizila
Monga ndimachita ine ooh
Fi ever lemme love ya
You di reason why I sing dis song
You loved me like my broda
Anthu ankatitenga amapasa
Koma chosencho unali lover
Ndiwe unali wapamtima wanga
Zikundiwawa poti tikusiyana
Ilo ndibodza loti sitimamvana
Shawty you're my best friend
You are unforgettable
I will never forget you
Sindingakuiwale (iiwale ee!!)
Zaiwe sindingaiwale
Ndizakukumbukila mpaka kale
Siunali bae chabe
Koma udali ngati m'bale
When I feel lonely unkandichezesa
Ndikakhumudwa unkandisekesa ah
Mi Seh I feel so lonely
Without you my baby
Ilo ndi bodza loti sitimamvana
Iwe ndi wanga tikamauzana
Ukamatalikila (ukamatalikila)
Uzindiganizila monga ndimachitila
Ukamatalikila uzindiganizila
Monga ndimachita ine ooh
Watch Video
About Good Bye
More EM SPECIAL Lyrics
Comments ( 0 )
No Comment yet
You May also Like
Get Afrika Lyrics Mobile App
About AfrikaLyrics
Follow Afrika Lyrics
© 2025, We Tell Africa Group Sarl