Kadigong Lyrics
...
Kadigong Lyrics by SHO MADJOZI
Moni moni moni
Kuyilowa ndi mutu
Ndasiya mudothi
Mayazi maya mayazi
Gwira malaya nane ndi ilowe basi
Mayazi mayazi mayazi
Kuyilowa ndi mutu mopanda manyazi
Maya mayazi mayazi
Nkhani yamanyado ilbe n’khala pakati
Mayazi mayazi mayazi
Okudya ndalama samatcheka balansi
Vina
Tchola
Tshika
Kadi gong
Sinali plani kuti ndikukonde (Koma)
watshekemela ngati ndiwe combe (Ona)
Watseleekeza ma guy wonse
odi ndi ka pote
Tizitchiiilla tiKhale Pa easy
Ndili ndi mandede ngati Iani lizzi
Ndimakoonda njonda zachimidzi
A/khale wauleemu opanda utchissi
Tenga u/moodzi tinyowe kukhosi
(Nane ndima/nyowa uka/kamba zaku\khosi )
Ndikutengele ku/Jhoni u/kawone tshotshi (jozi)**q
U/kazipeza /ndi achina Sho madJozi konkoo
Ndi/libe phuma ndine nkazi wodeekha
Koma ndi Kabwella undi/vulile wekha
Mfana woteentha ta/ziiyiteleka
ku/mayi chakulila ndika/mayi peleka
Vina
Tchola
Tshika
Kadi gong
Mkazi wakunja khalidwe lachimalawi
Ndipanga naye chani fukwa ndine mphawi
Nyumba yakwawo yaku mayadi
Makolo akachoka timapanga party
Chikondi cha season ngati mtengo wa mango
Koma ndatopa nane ndikhale wako
Uzi ndigwira gwira ngati kupanga chipako
Polama pango’no undigwiritse thako
Ndikukwatile kapena tipange chinkhoswe
Olo ndidzidya mwa chinsinsi ngati khoswe
Dona ya ulemu Ndipo alibe chipongwe
Ndimupatse mimba kuti akhale pakhonde
Wabwera ndi Bola odi ndikapote
Tikawone Nyanja Ng’ona ku liwonde
Kukunyaditsa kuti akuwone
A Nsanje ka
Watch Video
About Kadigong
More SHO MADJOZI Lyrics
Comments ( 0 )
No Comment yet
You May also Like
Get Afrika Lyrics Mobile App
About AfrikaLyrics
Follow Afrika Lyrics
© 2024, We Tell Africa Group Sarl